2 Mbiri 6:9 - Buku Lopatulika9 koma sudzandimangira nyumba ndiwe, koma mwana wako wakudzatuluka m'chuuno mwako, iyeyo adzalimangira dzina langa nyumbayi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 koma sudzandimangira nyumba ndiwe, koma mwana wako wakudzatuluka m'chuuno mwako, iyeyo adzalimangira dzina langa nyumbayi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Komabe si ndiwe udzamange nyumbayo, koma mwana wako wamwamuna amene udzabale, ndiye amene adzandimangire nyumba yomveketsa dzina langa.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Komatu si iwe amene udzamanga Nyumba ya Mulungu koma mwana wako, mwana amene iwe udzabereke. Iyeyo ndiye amene adzandimangire Nyumba.’ Onani mutuwo |