Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 6:8 - Buku Lopatulika

8 Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unachita bwino kuti unatero mumtima mwako;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unachita bwino kuti unatero mumtima mwako;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Koma Chautayo adauza Davide bambo wanga kuti, ‘Popeza unkaganiza mumtima mwako zoti undimangire nyumba, udachita bwino kumaganiza zimenezo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Koma Yehova ananena kwa abambo anga Davide kuti, ‘Popeza zinali mu mtima mwako kumangira Nyumba dzina langa, unachita bwino kukhala ndi maganizo amenewa mu mtima mwakomo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 6:8
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide atate wanga anafuna mumtima mwake kumangira dzina la Yehova Mulungu wa Israele nyumba.


koma sudzandimangira nyumba ndiwe, koma mwana wako wakudzatuluka m'chuuno mwako, iyeyo adzalimangira dzina langa nyumbayi.


Iye wachita chimene wakhoza; anandidzozeratu thupi langa ku kuikidwa m'manda.


Pakuti ngati chivomerezocho chili pomwepo, munthu alandiridwa monga momwe ali nacho, si monga chimsowa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa