Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 6:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo Davide atate wanga anafuna mumtima mwake kumangira dzina la Yehova Mulungu wa Israele nyumba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo Davide atate wanga anafuna mumtima mwake kumangira dzina la Yehova Mulungu wa Israele nyumba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Tsono mumtima mwake bambo wanga Davide ankaganiza zoti amange nyumba yomveketsa dzina la Chauta, Mulungu wa Aisraele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 “Abambo anga Davide anali ndi maganizo mu mtima mwawo oti amangire Nyumba Yehova Mulungu wa Israeli.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 6:7
7 Mawu Ofanana  

Mudziwa inu kuti atate wanga Davide sanathe kumangira dzina la Yehova Mulungu wake nyumba, chifukwa cha nkhondo zakumzinga konseko, mpaka atawaika Yehova pansi pa mapazi ake.


Ndipo Davide atate wanga anafuna m'mtima mwake kumangira dzina la Yehova Mulungu wa Israele nyumba.


Ndipo pokhala Davide m'nyumba mwake, Davideyo anati kwa Natani mneneri, Taona, ndikhala ine m'nyumba yamikungudza, koma likasa la chipangano la Yehova likhala m'nsalu zotchinga.


Ndipo Davide anati kwa Solomoni mwana wake, Kunena za ine, kumtima kwanga kudati, ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba.


Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unachita bwino kuti unatero mumtima mwako;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa