2 Mbiri 5:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti akerubi anafunyulula mapiko ao pamalo a likasa, ndi akerubi anaphimba likasa ndi mphiko zake pamwamba pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti akerubi anafunyulula mapiko ao pa malo a likasa, ndi akerubi anaphimba likasa ndi mphiko zake pamwamba pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Choncho akerubiwo ankatambasula mapiko ao pamwamba pa Bokosilo, kotero kuti ankaliphimba pamodzi ndi mphiko zake zonyamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Akerubiwo anatambalitsa mapiko awo pamwamba pa Bokosi la Chipangano ndipo anaphimba bokosilo pamodzi ndi mitengo yonyamulira. Onani mutuwo |