Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 5:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo amuna onse a Israele anasonkhana kwa mfumu kumadyerero anachitikawo, m'mwezi wachisanu ndi chiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo amuna onse a Israele anasonkhana kwa mfumu kumadyerero anachitikawo, m'mwezi wachisanu ndi chiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Aisraele onse adasonkhana pamaso pa mfumu nthaŵi ya chikondwerero cha mwezi wachisanu ndi chiŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ndipo Aisraeli onse anasonkhana pamaso pa mfumu nthawi ya chikondwerero cha mwezi wachisanu ndi chiwiri.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 5:3
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu onse a Israele anasonkhana kwa mfumu Solomoni kukadyerera m'mwezi wa Etanimu, ndiwo mwezi wachisanu ndi chiwiri.


Mwezi wachisanu ndi chiwiri, tsiku lakhumi ndi chisanu la mwezi, pachikondwerero, achite momwemo masiku asanu ndi awiri, monga mwa nsembe yauchimo, monga mwa nsembe yopsereza, ndi monga mwa nsembe yaufa, ndi monga mwa mafuta.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa