2 Mbiri 5:1 - Buku Lopatulika1 Momwemo zidatha ntchito zonse Solomoni adazichitira nyumba ya Yehova. Ndipo Solomoni anabwera nazo zopatulika zija za atate wake Davide; naziika siliva, ndi golide, ndi zipangizo zonse m'chuma cha nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Momwemo zidatha ntchito zonse Solomoni adazichitira nyumba ya Yehova. Ndipo Solomoni anabwera nazo zopatulika zija za atate wake Davide; naziika siliva, ndi golide, ndi zipangizo zonse m'chuma cha nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Motero Solomoni adatsiriza ntchito zonse za ku Nyumba ya Mulungu. Tsono adabwera ndi zinthu zonse zimene Davide bambo wake adaazipereka, ndipo adaika siliva, golide ndi ziŵiya zonse m'zipinda zosungiramo chuma cha ku Nyumba ya Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pamene ntchito yonse imene Solomoni anagwira pa Nyumba ya Yehova inatha, anabwera ndi zinthu zonse zimene abambo ake Davide anazipereka; siliva, golide ndi ziwiya. Anaziyika mʼzipinda zosungiramo chuma cha ku Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwo |