2 Mbiri 4:5 - Buku Lopatulika5 Ndi kuchindikira kwake kunanga chikhato, ndi mlomo wake unasadamuka ngati mlomo wa chomwera, ngati duwa la kakombo; analowamo madzi a mitsuko yaikulu zikwi zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndi kuchindikira kwake kunanga chikhato, ndi mlomo wake unasadamuka ngati mlomo wa chomwera, ngati luwa la kakombo; analowamo madzi a mitsuko yaikulu zikwi zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Thankilo kuchindikira kwake kunali ngati chikhatho. M'milomo mwake munkaoneka ngati m'milomo mwa chikho, ngati duŵa la kakombo. Munkaloŵa madzi okwanira malitara 60,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mbiyayo inali yochindikala ngati chikhatho ndipo mkombero wake unali ngati mkombero wa chikho, ngati duwa lokongola kwambiri. Mʼmbiyamo munkalowa madzi okwana malita 60,000. Onani mutuwo |