2 Mbiri 4:12 - Buku Lopatulika12 nsanamira ziwiri, ndi zikhozo, ndi mitu iwiri inali pamwamba pa nsanamirazo, ndi maukonde awiri akukuta zikho ziwiri za mitu ili pamwamba pa nsanamirazo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 nsanamira ziwiri, ndi zikhozo, ndi mitu iwiri inali pamwamba pa nsanamirazo, ndi maukonde awiri akukuta zikho ziwiri za mitu ili pamwamba pa nsanamirazo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 ndiye kuti kumanga nsanamira ziŵiri zija, kupanga makapotolosi aŵiri aja okhala pamwamba pa nsanamirazo, ndiponso maukonde aŵiri aja ophimba ziwaya ziŵiri zija za kunsonga kwa makapotolosi aja okhala pamwamba pa nsanamira. Adapanganso maukonde aŵiri ovundikira pamwamba pa mbale ziŵiri za pa mitu imene inali pamwamba pa nsanamira ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Nsanamira ziwiri; mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; maukonde awiri okongoletsera mbale ziwiri za mitu yapamwamba pa nsanamirazo; Onani mutuwo |