2 Mbiri 4:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Huramu anapanga miphika, ndi zoolera zake, ndi mbale zowazira zake. Natsiriza Huramu ntchito adaichitira mfumu Solomoni m'nyumba ya Mulungu: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Huramu anapanga miphika, ndi zoolera zake, ndi mbale zowazira zake. Natsiriza Huramu ntchito adaichitira mfumu Solomoni m'nyumba ya Mulungu: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Huramu adapanganso mikhate, mafosholo ndi mabeseni ambiri. Motero Huramu adamatsiriza ntchito ya Nyumba ya Chauta imene ankagwirira mfumu Solomoni: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iye anapanganso miphika ndi mafosholo ndi mabeseni owazira magazi. Kotero Hiramu anatsiriza ntchito yonse ya ku Nyumba ya Mulungu imene ankagwirira Mfumu Solomoni: Onani mutuwo |