Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 4:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo anaika thawalelo ku dzanja lamanja la nyumba kum'mawa chakumwera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo anaika thawalelo ku dzanja lamanja la nyumba kum'mawa chakumwera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ndipo adaika thanki lija pa ndonyo yakumwera ya Nyumbayo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Anayika mbiya ija mbali yakummwera pamene mbali ya kummawa ndi kummwera zimakumana.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 4:10
2 Mawu Ofanana  

Ndipo panali, asanathe kunena, taonani, anatuluka Rebeka, amene anambala Betuele, mwana wamwamuna wa Milika, mkazi wa Nahori mphwake wa Abrahamu, ndi mtsuko wake paphewa pake.


Ndipo anaika maphaka asanu ku dzanja lamanja la nyumba, ndi maphaka asanu ku dzanja lamanzere la nyumba; naika thawalelo ku dzanja lamanja la nyumba kum'mawa kupenya kumwera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa