2 Mbiri 32:6 - Buku Lopatulika6 Naika akazembe a nkhondo alamulire anthu, nawasonkhanitsira kuli iye kubwalo la kuchipata cha mzinda, nanena nao motonthoza mtima wao ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Naika akazembe a nkhondo alamulire anthu, nawasonkhanitsira kuli iye kubwalo la kuchipata cha mudzi, nanena nao motonthoza mtima wao ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono adaika atsogoleri ankhondo kuti azilamula anthu, naŵasonkhanitsa anthuwo pa bwalo ku chipata cha mzindawo. Tsono adaŵalankhula moŵalimbitsa mtima kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye anasankha atsogoleri a ankhondo olamulira anthu ndipo anawasonkhanitsa pamaso pake pa bwalo la chipata cha mzinda ndi kuwalimbikitsa ndi mawu awa: Onani mutuwo |