Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 32:10 - Buku Lopatulika

10 Atero Senakeribu mfumu ya Asiriya, Mutama chiyani kuti mukhala m'linga mu Yerusalemu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Atero Senakeribu mfumu ya Asiriya, Mutama chiyani kuti mukhala m'linga m'Yerusalemu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 “Senakeribu, mfumu ya ku Asiriya, akufunsa kuti, ‘Kodi mukukhulupirira chiyani, kuti muzikanirira mu Yerusalemu ndi kumatsekedwa?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 “Senakeribu mfumu ya ku Asiriya akuti: Kodi inu mukukhulupirira chiyani, kuti mukukhalabe mu Yerusalemu mutazingidwa?

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 32:10
4 Mawu Ofanana  

Nanena nao kazembeyo, Muuzetu Hezekiya, Itero mfumu yaikulu, mfumu ya Asiriya, Chikhulupiriro ichi nchotani uchikhulupirira?


Sakukopani Hezekiya, kuti akuperekeni mufe nayo njala ndi ludzu, ndi kuti, Yehova Mulungu wathu adzatilanditsa m'dzanja la mfumu ya Asiriya?


Pambuyo pake Senakeribu mfumu ya Asiriya, akali ku Lakisi ndi mphamvu yake yonse pamodzi naye, anatuma anyamata kwa Hezekiya mfumu ya Yuda, ndi kwa Ayuda onse okhala ku Yerusalemu, ndi kuti,


Ndipo kazembeyo anati kwa iwo, Nenani inu tsopano kwa Hezekiya, Itero mfumu yaikulu, mfumu ya Asiriya, Kodi chikhulupiriro ichi nchotani, uchikhulupirira iwe?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa