Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 30:2 - Buku Lopatulika

2 Pakuti mfumu idapangana ndi akulu ake, ndi msonkhano wonse wa mu Yerusalemu, kuti achite Paska mwezi wachiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Pakuti mfumu idapangana ndi akulu ake, ndi msonkhano wonse wa m'Yerusalemu, kuti achite Paska mwezi wachiwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Pakuti mfumu, nduna zake ndi anthu onse a ku Yerusalemu anali atapangana kuti azichita Paska pa mwezi wachiŵiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Mfumu ndi akuluakulu ake pamodzi ndi anthu onse a mu Yerusalemu anagwirizana kuti akondwerere Paska pa mwezi wachiwiri.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 30:2
11 Mawu Ofanana  

Zedi silinachitike Paska lotere chiyambire masiku a oweruza anaweruza Israele, ngakhale m'masiku a mafumu a Israele, kapena mafumu a Yuda;


Ndipo Solomoni analankhula ndi Aisraele onse, ndi akulu a zikwi ndi a mazana, ndi kwa oweruza, ndi kwa kalonga aliyense wa Israele, akulu a nyumba za makolo.


Ndipo Hezekiya anatumiza kwa Israele ndi Yuda onse, nalembanso makalata kwa Efuremu ndi Manase, kuti abwere kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu, kuchitira Yehova Mulungu wa Israele Paska.


Nasonkhana ku Yerusalemu anthu ambiri kuchita chikondwerero cha Mkate wopanda chotupitsa mwezi wachiwiri, msonkhano waukulu ndithu.


Pamenepo anaphera Paska tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi wachiwiri, ndipo ansembe ndi Alevi anachita manyazi, nadzipatula, nabwera nazo nsembe zopsereza kunyumba ya Yehova.


Pamenepo Yosiya anachitira Yehova Paska mu Yerusalemu, naphera Paska tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi woyamba.


Popanda upo wanzeru anthu amagwa; koma pochuluka aphungu pali chipulumutso.


Zolingalira zizimidwa popanda upo; koma pochuluka aphungu zikhazikika.


Mnyamata wosauka ndi wanzeru apambana mfumu yokalamba ndi yopusa, imene sifunanso kulangidwa mwambo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa