2 Mbiri 3:9 - Buku Lopatulika9 Ndi kulemera kwake kwa misomali ndiko masekeli makumi asanu a golide. Ndipo anazikuta ndi golide zipinda zosanjikizana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi kulemera kwake kwa misomali ndiko masekeli makumi asanu a golide. Ndipo anazikuta ndi golide zipinda zosanjikizana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Magaramu 570 a golide adaŵagwiritsa ntchito kupanga misomali. Ndipo zipinda zapamwamba adazikutanso ndi golide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Misomali yagolide imalemera magalamu 570. Anakutanso ndi golide zipinda zapamwamba. Onani mutuwo |