2 Mbiri 3:7 - Buku Lopatulika7 Anamamatizanso Kachisi, mitanda, ziundo, ndi makoma ake, ndi zitseko zake, ndi golide; nalemba akerubi pamakoma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Anamamatizanso Kachisi, mitanda, ziundo, ndi makoma ake, ndi zitseko zake, ndi golide; nalemba akerubi pamakoma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Motero adaikuta nyumba yonseyo ndi golide, ndiye kuti mitanda yake, ziwundo zake, makoma ake ndi zitseko zake zomwe. Ndipo adazokota zithunzi za akerubi pa makoma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye anakutira ndi golide mitanda ya ku denga, maferemu a zitseko, makoma ndi zitseko za Nyumba ya Mulungu, ndipo anajambula Akerubi mʼmakoma mwake. Onani mutuwo |