2 Mbiri 3:13 - Buku Lopatulika13 Mapiko a akerubi awa anafunyululika mikono makumi awiri; ndipo anaima ndi mapazi ao, ndi nkhope zao zinaloza kukhomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Mapiko a akerubi awa anafunyululika mikono makumi awiri; ndipo anaima ndi mapazi ao, ndi nkhope zao zinaloza kukhomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mapiko a akerubi amenewo onse pamodzi akaŵatambasula ankakwanira mamita asanu ndi anai. Akerubiwo adaaimirira pa mapazi ao, kuyang'ana m'kati mwa nyumbayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mapiko a Akerubiwa akawatambasula amatalika mamita asanu ndi anayi. Akerubiwa anayimirira pa mapazi awo, kuyangʼana chipinda chachikulu. Onani mutuwo |