2 Mbiri 3:12 - Buku Lopatulika12 Ndi phiko la kerubi wina mikono isanu lojima khoma la nyumba, ndi phiko linzake mikono isanu lolumikizana ndi phiko la kerubi wina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndi phiko la kerubi wina mikono isanu lojima khoma la nyumba, ndi phiko linzake mikono isanu lolumikizana ndi phiko la kerubi wina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndipo Kerubi ameneyu phiko lake limodzi, la mamita aŵiri nkanthu, linkakhudza ku khoma la nyumba, phiko lake lina, nalonso la mamita aŵiri nkanthu, lidalumikizana ndi phiko la kerubi woyamba uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Chimodzimodzinso phiko la Kerubi wachiwiri linali loposerapo mamita awiri ndipo limakhudza mbali ina ya khoma la Nyumba ya Mulungu, ndipo linalo limene linalinso loposera mamita awiri, limakhudza phiko la Kerubi woyamba uja. Onani mutuwo |