Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 3:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo m'malo opatulika kwambiri anapanga akerubi awiri, anachita osema, nawakuta ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo m'malo opatulika kwambiri anapanga akerubi awiri, anachita osema, nawakuta ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ku malo opatulika kwambiriko adapangako akerubi aŵiri achitsulo, ndipo adaŵakuta ndi golide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ku Malo Opatulika Kwambiri iye anapangako Akerubi awiri achitsulo ndipo anawakuta ndi golide.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 3:10
4 Mawu Ofanana  

Ndi mapiko a akerubi m'litali mwake ndimo mikono makumi awiri; phiko la kerubi mmodzi mikono isanu, lojima khoma la nyumba; ndi phiko linzake mikono isanu, lokhudzana nalo phiko la kerubi wina.


Uzipanganso akerubi awiri agolide; uwasule mapangidwe ake, pa mathungo ake awiri a chotetezerapo.


Ndipo akerubi afunyululire mapiko ao m'mwamba, ndi kuphimba chotetezerapo ndi mapiko ao, ndi nkhope zao zipenyane; nkhope za akerubi zipenye kuchotetezerapo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa