2 Mbiri 27:8 - Buku Lopatulika8 Anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Anali wa zaka makumi awiri mphambu zisanu polowa ufumu wake, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka khumi mphambu zisanu ndi chimodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Iyeyo anali wa zaka 25 pamene ankaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 16 ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka 16. Onani mutuwo |