2 Mbiri 27:7 - Buku Lopatulika7 Machitidwe ena tsono a Yotamu, ndi nkhondo zake zonse, ndi njira zake, taonani, zalembedwa m'buku la mafumu a Israele ndi Yuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Machitidwe ena tsono a Yotamu, ndi nkhondo zake zonse, ndi njira zake, taonani, zalembedwa m'buku la mafumu a Israele ndi Yuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono ntchito zonse za Yotamu, ndi nkhondo zake zonse ndiponso makhalidwe ake, zidalembedwa m'buku la mafumu a ku Israele ndi mafumu a ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Zina ndi zina zokhudza ulamuliro wa Yotamu, kuphatikizapo nkhondo zake zonse ndi zinthu zina zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mafumu a Israeli ndi Yuda. Onani mutuwo |