2 Mbiri 27:4 - Buku Lopatulika4 Namanga mizinda m'mapiri a Yuda, ndi m'nkhalango anamanga nyumba zansanja, ndi nsanja zomwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Namanga midzi m'mapiri a Yuda, ndi m'nkhalango anamanga nyumba zansanja, ndi nsanja zomwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Komanso adamanga mizinda ku dziko lonse lamapiri la Yuda. Adamanganso malinga ndi nsanja ku nkhalango zakumapiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iye anamanga mizinda mʼmapiri a ku Yuda ndipo anamanganso malinga ndi nsanja mʼmadera a ku nkhalango. Onani mutuwo |