2 Mbiri 27:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anachita zoongoka pamaso pa Yehova, monga umo adachitira atate wake Uziya; pokhapo sanalowe mu Kachisi wa Yehova. Koma anthu anachitabe zovunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anachita zoongoka pamaso pa Yehova, monga umo adachitira atate wake Uziya; pokhapo sanalowe m'Kachisi wa Yehova. Koma anthu anachitabe zovunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Iyeyo adachita zolungama pamaso pa Chauta, kutsata zonse zimene ankachita Uziya, bambo wake, kupatula kuti sadakaloŵe mwamphamvu ku Nyumba ya Chauta. Koma anthu ankachitabe zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anachita zolungama pamaso pa Yehova, monga anachitira Uziya abambo ake, kupatula kuti iyeyo sanalowe mʼNyumba ya Yehova. Komabe anthu anapitirira kuchita zoyipa. Onani mutuwo |