2 Mbiri 26:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Azariya wansembe analowa pambuyo pake, ndi pamodzi naye ansembe a Yehova makumi asanu ndi atatu, ndiwo olimba mtima; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Azariya wansembe analowa pambuyo pake, ndi pamodzi naye ansembe a Yehova makumi asanu ndi atatu, ndiwo olimba mtima; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma wansembe Azariya adaloŵa pambuyo pa iyeyo, pamodzi ndi ansembe a Chauta 80 olimba mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Wansembe Azariya pamodzi ndi ansembe a Yehova ena 80 olimba mtima anamutsatira. Onani mutuwo |