2 Mbiri 26:11 - Buku Lopatulika11 Uziya anali nalonso khamu la anthu a nkhondo, otuluka kunkhondo magulu; nawawerenga monga mwa mawerengedwe ao ndi dzanja la mlembi Yeiyele, ndi kapitao Maaseiya, monga anawauza Hananiya kazembe wina wa mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Uziya anali nalonso khamu la anthu a nkhondo, otuluka kunkhondo magulu; nawawerenga monga mwa mawerengedwe ao ndi dzanja la mlembi Yeiyele, ndi kapitao Maaseiya, monga anawauza Hananiya kazembe wina wa mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Komanso Uziyayo anali ndi gulu la asilikali odziŵa nkhondo. Anali m'magulumagulu potsata dongosolo limene adaalikonza mlembi Yeiyele ndi Maaseiya, mkulu wankhondo. Amene ankaŵalamulira asilikaliwo anali Hananiya, mmodzi mwa nduna za mfumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Uziya anali ndi gulu lankhondo lophunzitsidwa bwino, lokonzekera kupita ku nkhondo mʼmagulu monga mwa chiwerengero chawo chimene mlembi Yeiyeli ndi Maaseya anasonkhanitsa motsogozedwa ndi Hananiya mmodzi mwa akuluakulu a mfumu. Onani mutuwo |