Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 25:3 - Buku Lopatulika

3 Kunachitika tsono, utamkhazikikira ufumu, anapha anyamata ake amene adapha mfumu atate wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Kunachitika tsono, utamkhazikikira ufumu, anapha anyamata ake amene adapha mfumu atate wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Tsono atangolandira mphamvu zonse zaufumu m'manja mwake, adapha anyamata ake amene adaapha mfumu ija, bambo wake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Pamene mphamvu zonse zaufumu zinali mʼmanja mwake, iye anapha akuluakulu amene anapha abambo ake, mfumu ija.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 25:3
8 Mawu Ofanana  

Atauka tsono Yehoramu mu ufumu wa atate wake, nadzilimbitsa, anapha ndi lupanga abale ake onse, ndi akalonga ena omwe a Israele.


Koma sanaphe ana ao, koma anachita monga umo mulembedwa m'chilamulo, m'buku la Mose, monga Yehova analamulira, ndi kuti, Atate asafere ana, ndi ana asafere atate; koma yense afere tchimo lakelake.


Koma anthu a m'dziko anapha onse adampangira chiwembu mfumu Amoni; ndi anthu a m'dziko analonga Yosiya mwana wake akhale mfumu m'malo mwake.


Koma munthu akachita dala pa mnzake, kumupha monyenga; uzimchotsa ku guwa langa la nsembe, kuti afe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa