2 Mbiri 24:9 - Buku Lopatulika9 Nalalikira mwa Yuda ndi Yerusalemu, abwere nao kwa Yehova msonkho umene Mose mtumiki wa Mulungu anauikira Aisraele m'chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Nalalikira mwa Yuda ndi Yerusalemu, abwere nao kwa Yehova msonkho umene Mose mtumiki wa Mulungu anauikira Aisraele m'chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo adalengeza kwa anthu onse a ku Yuda ndi a mu Yerusalemu, kuti adzapereke kwa Chauta ndalama zimene Mose mtumiki wa Mulungu adaalamula kuchipululu kuja kuti Aisraele onse azipereka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo analengeza kwa anthu a mu Yuda ndi mu Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho umene Mose mtumiki wa Mulungu analamulira Aisraeli mʼchipululu. Onani mutuwo |