2 Mbiri 24:8 - Buku Lopatulika8 Nilamulira mfumu, ndipo anapanga bokosi, naliika kunja kuchipata cha nyumba ya Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Nilamulira mfumu, ndipo anapanga bokosi, naliika kunja kuchipata cha nyumba ya Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Motero mfumu idalamula kuti apange bokosi, aliike panja pa khomo la Nyumba ya Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mfumu italamulira, bokosi linapangidwa ndipo linayikidwa panja pa chipata cha Nyumba ya Yehova. Onani mutuwo |