Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 24:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo pambuyo pake mumtima mwa Yowasi munali chofuna kukonzanso nyumba ya Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo pambuyo pake mumtima mwa Yowasi munali chofuna kukonzanso nyumba ya Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Pambuyo pake Yowasi adatsimikiza zokonzanso Nyumba ya Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Patapita nthawi Yowasi anatsimikiza zokonzanso Nyumba ya Yehova.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 24:4
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo ao, natumikira zifanizo, ndi mafano; ndipo mkwiyo unawagwera Yuda ndi Yerusalemu, chifukwa cha kupalamula kwao kumene.


Ndipo Yehoyada anamtengera akazi awiri, nabala ana aamuna ndi aakazi.


Pakuti ana a Ataliya mkazi woipa uja anathyola chitseko cha nyumba ya Mulungu, natenga zopatulidwa zonse za nyumba ya Yehova kuzipereka kwa Baala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa