Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 24:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo Yehoyada anamtengera akazi awiri, nabala ana aamuna ndi aakazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo Yehoyada anamtengera akazi awiri, nabala ana aamuna ndi aakazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Yehoyada adaipezera mfumuyo akazi aŵiri, ndipo idabereka ana aamuna ndi ana aakazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Yehoyada anamupezera iye akazi awiri, ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 24:3
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anakhala m'chipululu cha Parani; ndipo amake anamtengera iye mkazi wa ku dziko la Ejipito.


Koma udzanke ku dziko langa, kwa abale anga, ndi kumtengera mwana wanga Isaki mkazi.


Ndipo Lameki anadzitengera yekha akazi awiri: dzina lake la wina ndi Ada, dzina lake la mnzake ndi Zila.


Koma Yehoyada anakalamba, nachuluka masiku, namwalira iye; ndiye wa zaka zana limodzi mphambu makumi atatu pamene anamwalira.


Ndipo Yowasi anachita zoongoka pamaso pa Yehova masiku onse a Yehoyada wansembe.


Ndipo pambuyo pake mumtima mwa Yowasi munali chofuna kukonzanso nyumba ya Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa