2 Mbiri 24:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yowasi anachita zoongoka pamaso pa Yehova masiku onse a Yehoyada wansembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yowasi anachita zoongoka pamaso pa Yehova masiku onse a Yehoyada wansembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono Yowasiyo adachita zolungama pamaso pa Chauta nthaŵi yonse ya moyo wa wansembe Yehoyada. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yowasi anachita zolungama pamaso pa Yehova nthawi yonse ya moyo wa wansembe Yehoyada. Onani mutuwo |
Koma wolungamayo akabwerera kuleka chilungamo chake, nakachita mphulupulu, ndi kuchita monga mwa zonyansa zonse azichita woipa, adzakhala ndi moyo kodi? Nnena chimodzi cha zolungama zake zonse adzazichita chidzakumbukika m'kulakwa kwake analakwa nako, ndi m'kuchimwa kwake anachimwa nako; momwemo adzafa.