2 Mbiri 24:1 - Buku Lopatulika1 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wake, nakhala mfumu mu Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la make ndiye Zibiya wa ku Beereseba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wake, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la make ndiye Zibiya wa ku Beereseba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziŵiri pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka 40 ku Yerusalemu. Mai wake anali Zibiya wa ku Beereseba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yowasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri pamene anakhala mfumu, ndipo analamulira mu Yerusalemu kwa zaka makumi anayi. Dzina la amayi ake linali Zibiya wa ku Beeriseba. Onani mutuwo |