2 Mbiri 23:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Alevi amzinge mfumu pozungulirapo, yense ndi zida zake m'dzanja mwake; ndipo aliyense wolowa m'nyumba aphedwe; nimukhale inu pamodzi ndi mfumu pakulowa ndi pakutuluka iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Alevi amzinge mfumu pozungulirapo, yense ndi zida zake m'dzanja mwake; ndipo aliyense wolowa m'nyumba aphedwe; nimukhale inu pamodzi ndi mfumu pakulowa ndi pakutuluka iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Alevi akhale moizungulira mfumu, aliyense atatenga zida m'manja. Wina aliyense amene ati aloŵe m'Nyumbamo aphedwe. Muzikhala nayo mfumu kulikonse kumene iziyenda.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Alevi akhale mozungulira mfumu, munthu aliyense ali ndi chida chake mʼmanja. Aliyense amene alowe mʼNyumba ya Mulungu ayenera kuphedwa. Mukhale nayo pafupi mfumu kulikonse kumene izipita.” Onani mutuwo |