2 Mbiri 23:1 - Buku Lopatulika1 Koma chaka chachisanu ndi chiwiri Yehoyada anadzilimbitsa natenga atsogoleri a mazana, Azariya mwana wa Yerohamu, ndi Ismaele mwana wa Yehohanani, ndi Azariya mwana wa Obedi, ndi Maaseiya mwana wa Adaya, ndi Elisafati mwana wa Zikiri, apangane naye pamodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma chaka chachisanu ndi chiwiri Yehoyada anadzilimbitsa natenga atsogoleri a mazana, Azariya mwana wa Yerohamu, ndi Ismaele mwana wa Yehohanani, ndi Azariya mwana wa Obedi, ndi Maaseiya mwana wa Adaya, ndi Elisafati mwana wa Zikiri, apangane naye pamodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Koma pa chaka chachisanu ndi chiŵiri, wansembe Yehoyada adalimba mtima, naitana anthu aŵa, amene anali atsogoleri a anthu mazana: Azariya, mwana wa Yerohamu, Ismaele mwana wa Yehohanani, Azariya mwana wa Obedi, Maaseiya mwana wa Adaya ndi Elisafati mwana wa Zikiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mʼchaka chachisanu ndi chiwiri Yehoyada anaonetsa mphamvu zake. Iye anachita pangano ndi olamulira magulu a anthu 100: Azariya mwana wa Yerohamu, Ismaeli mwana wa Yehohanani, Azariya mwana wa Obedi, Maaseya mwana wa Adaya ndi Elisafati mwana wa Zikiri. Onani mutuwo |