2 Mbiri 22:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo kunali, pakulanga Yehu nyumba ya Ahabu, anapeza akalonga a Yuda, ndi ana a abale a Ahaziya, akutumikira Ahaziya, nawapha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo kunali, pakulanga Yehu nyumba ya Ahabu, anapeza akalonga a Yuda, ndi ana a abale a Ahaziya, akutumikira Ahaziya, nawapha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Pamene Yehu ankalanga banja la Ahabu lija, adakumana ndi atsogoleri a ku Yuda ndiponso ana aamuna a abale ake a Ahaziya, amene ankatumikira Ahaziya, iye nkuŵapha onsewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pamene Yehu ankalanga banja la Ahabu anapeza atsogoleri a ku Yuda ndiponso ana aamuna a abale ake a Ahaziya amene amatumikira Ahaziya, ndipo anawapha. Onani mutuwo |