2 Mbiri 21:5 - Buku Lopatulika5 Yehoramu anali wa zaka makumi atatu mphambu ziwiri polowa ufumu wake, nachita ufumu mu Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Yehoramu anali wa zaka makumi atatu mphambu ziwiri polowa ufumu wake, nachita ufumu m'Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Yehoramu anali wa zaka 32 pamene adaloŵa ufumu, ndipo adalamulira zaka zisanu ndi zitatu ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yehoramu anali wa zaka 32 pamene anakhala mfumu, ndipo analamulira mu Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu. Onani mutuwo |