2 Mbiri 21:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo atate wao anawapatsa mphatso zazikulu, zasiliva, ndi zagolide, ndi za mtengo wake, pamodzi ndi mizinda yamalinga mu Yuda; koma ufumu anauninkha kwa Yehoramu; pakuti ndiye mwana wake woyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo atate wao anawapatsa mphatso zazikulu, zasiliva, ndi zagolide, ndi za mtengo wake, pamodzi ndi midzi yamalinga m'Yuda; koma ufumu anauninkha kwa Yehoramu; pakuti ndiye mwana wake woyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Atate ao adaaŵapatsa mphatso zambiri za siliva, golide, ndi zinthu zamtengowapatali, pamodzi ndi mizinda yamalinga ya ku Yuda. Koma ufumu adapatsa Yehoramu, chifukwa chakuti anali mwana wachisamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Abambo awo anawapatsa mphatso zambiri za siliva, golide ndi zinthu zina zamtengowapatali komanso mizinda yotetezedwa ya Yuda. Koma iye anapereka ufumu kwa Yehoramu chifukwa anali mwana wake woyamba kubadwa. Onani mutuwo |