2 Mbiri 21:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake, naikidwa pamodzi ndi makolo ake m'mzinda wa Davide; ndi Yehoramu mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ake, naikidwa pamodzi ndi makolo ake m'mudzi wa Davide; ndi Yehoramu mwana wake anakhala mfumu m'malo mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yehosafati adamwalira, naikidwa m'manda momwe adaaikidwa makolo akewo mu mzinda wa Davide. Tsono Yehoramu mwana wake adaloŵa ufumu m'malo mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehosafati anamwalira nayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake mu mzinda wa Davide. Ndipo Yehoramu mwana wake analowa ufumu mʼmalo mwake. Onani mutuwo |