Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 20:16 - Buku Lopatulika

16 Mawa muwatsikire; taonani, akwera pokwerera pa Zizi, mudzakomana nao polekezera chigwa chakuno cha chipululu cha Yeruwele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Mawa muwatsikire; taonani, akwera pokwerera pa Zizi, mudzakomana nao polekezera chigwa chakuno cha chipululu cha Yeruwele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Maŵa mupite mukamenyane nawo nkhondo. Adzabwera ndipo adzadzera cha ku chikwera cha Zizi. Mudzaŵapeza pafupi ndi chigwa cha kuvuma kwa chipululu cha Yeruwele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Mawa mupite mukamenyane nawo. Adzakhala akubwera mokweza kudzera Njira ya Zizi, ndipo mukawapeza kumapeto kwa chigwa cha ku chipululu cha Yeruweli.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 20:16
3 Mawu Ofanana  

nati iye, Tamverani Ayuda inu nonse, ndi inu okhala mu Yerusalemu, ndi inu mfumu Yehosafati, atero nanu Yehova, Musaope musatenge nkhawa chifukwa cha aunyinji ambiri awa; pakuti nkhondoyi si yanu, koma ya Mulungu.


Si kwanu kuchita nkhondo kuno ai; chilimikani, imani, nimupenye chipulumutso cha Yehova pa inu Yuda ndi Yerusalemu; musaope, kapena kutenga nkhawa; mawa muwatulukire, popeza Yehova ali ndi inu.


Koma Yehova anati kwa Yoswa, Usaope chifukwa cha iwowa; pakuti mawa, dzuwa lino ndidzawapereka onse ophedwa pamaso pa Israele; udzawadula mitsindo akavalo ao, ndi kutentha agaleta ao ndi moto.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa