2 Mbiri 2:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anaika zikwi makumi asanu ndi awiri za iwowa asenze mirimo, ndi zikwi makumi asanu ndi atatu ateme m'mapiri, ndi akapitao zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi agwiritse anthu ntchito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anaika zikwi makumi asanu ndi awiri za iwowa asenze mirimo, ndi zikwi makumi asanu ndi atatu ateme m'mapiri, ndi akapitao zikwi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi agwiritse anthu ntchito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adapatula anthu 70,000 kuti akhale amtengatenga, ndipo anthu 80,000 kuti akhale okumba miyala ku mapiri. Tsono anthu 3,600 adaŵaika kuti akhale akapitao ogwiritsa anthu ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iye anayika anthu 70,000 kuti akhale onyamula katundu ndi anthu 80,000 kuti akhale ophwanya miyala mʼmapiri, anthu 3,600 anawayika kukhala akapitawo oyangʼanira anthu pa ntchitoyo. Onani mutuwo |