2 Mbiri 2:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Huramu mfumu ya Tiro anayankha ndi kulembera, natumiza kalatayo kwa Solomoni, ndi kuti, Powakonda anthu ake Yehova anakulongani mfumu yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Huramu mfumu ya Tiro anayankha ndi kulembera, natumiza kalatayo kwa Solomoni, ndi kuti, Powakonda anthu ake Yehova anakulongani mfumu yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono Hiramu, mfumu ya ku Tiro, adayankha Solomoni pomulembera kalata yonena kuti, “Chifukwa chakuti Chauta amakonda anthu ake, wakuika iweyo kuti ukhale mfumu yao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Hiramu, mfumu ya ku Turo, anamuyankha Solomoni pomulembera kalata kuti, “Chifukwa Yehova amakonda anthu ake, wayika iwe kukhala mfumu yawo.” Onani mutuwo |