2 Mbiri 18:6 - Buku Lopatulika6 Koma Yehosafati anati, Kulibenso kuno mneneri wa Yehova, kuti tifunsire kwa iye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma Yehosafati anati, Kulibenso kuno mneneri wa Yehova, kuti tifunsire kwa iye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma Yehosafati adafunsa kuti, “Kodi pano palibe mneneri wina wa Chauta woti tipempheko nzeru?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma Yehosafati anafunsanso kuti, “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova amene ife tingafunsireko?” Onani mutuwo |