Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 17:8 - Buku Lopatulika

8 ndi pamodzi nao Alevi, ndiwo Semaya, ndi Netaniya, ndi Zebadiya, ndi Asahele, ndi Semiramoti, ndi Yehonatani, ndi Adoniya, ndi Tobiya, ndi Tobadoniya, Alevi; ndi pamodzi nao Elisama ndi Yehoramu, ansembe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndi pamodzi nao Alevi, ndiwo Semaya, ndi Netaniya, ndi Zebadiya, ndi Asahele, ndi Semiramoti, ndi Yehonatani, ndi Adoniya, ndi Tobiya, ndi Tobadoniya, Alevi; ndi pamodzi nao Elisama ndi Yehoramu, ansembe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Adapita ndi Alevi aŵa: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asahele, Semiramoti, Yohonatani, Adoniya, Tobiya ndi Tobadoniya. Alevi ameneŵa anali pamodzi ndi ansembe aŵa: Elisama ndi Yehoramu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Pamodzi ndi iwo panali Alevi ena: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yonatani, Adoniya, Tobiya ndi Tobu-Adoniya ndiponso ansembe Elisama ndi Yehoramu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 17:8
4 Mawu Ofanana  

Yehosafati anaikanso mu Yerusalemu Alevi, ndi ansembe ena, ndi akulu a nyumba za makolo mu Israele, aweruzire Yehova, nanena milandu. Ndipo anabwerera kudza ku Yerusalemu.


Nati kwa Alevi akuphunzitsa Aisraele onse, ndiwo opatulikira Yehova, Ikani likasa lopatulika m'nyumba imene Solomoni mwana wa Davide mfumu ya Israele anaimanga; silikhalanso katundu pa mapewa anu; tsopano mutumikire Yehova Mulungu wanu, ndi anthu ake Israele.


Pakuti milomo ya wansembe iyenera kusunga chidziwitso, ndi anthu ayenera kufunafuna chilamulo pakamwa pake; pakuti iye ndiye mthenga wa Yehova wa makamu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa