2 Mbiri 17:2 - Buku Lopatulika2 Naika ankhondo m'mizinda yonse yamalinga ya Yuda, naika aboma m'dziko la Yuda, ndi m'mizinda ya Efuremu, imene adailanda Asa atate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Naika ankhondo m'midzi yonse yamalinga ya Yuda, naika aboma m'dziko la Yuda, ndi m'midzi ya Efuremu, imene adailanda Asa atate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adaika magulu ankhondo ku mizinda yonse yamalinga ya ku Yuda, ndipo adamanga maboma ankhondo ku dziko la Yuda ndi ku mizinda ya ku Efuremu, imene Asa bambo wake adailanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anayika magulu a asilikali mʼmizinda yonse yotetezedwa ya Yuda, ndipo anamanga maboma mu Yuda ndi mʼmizinda yonse ya Efereimu imene Asa abambo ake analanda. Onani mutuwo |