2 Mbiri 17:13 - Buku Lopatulika13 Nakhala nazo ntchito zambiri m'mizinda ya Yuda, ndi anthu a nkhondo, ngwazi zamphamvu mu Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Nakhala nazo ntchito zambiri m'midzi ya Yuda, ndi anthu a nkhondo, ngwazi zamphamvu m'Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Choncho anali ndi nyumba zikuluzikulu zosungiramo zinthu ku mizinda ya ku Yuda. Ku Yerusalemu anali ndi ankhondo, anthu amphamvu ndi olimba mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 ndipo anali ndi katundu wambiri mʼmizinda ya Yuda. Iye anayikanso asilikali odziwa bwino nkhondo mu Yerusalemu. Onani mutuwo |