Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 16:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo kunali, pakumva ichi Baasa, analeka kumangitsa Rama, naleketsa ntchito yake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo kunali, pakumva ichi Baasa, analeka kumangitsa Rama, naleketsa ntchito yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Tsono Baasa atazimva zimenezi, adaleka kumangira Rama linga ndipo ntchito yonseyo adaisiya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Baasa atamva izi, anasiya kumanga Rama ndipo anayimitsa ntchito yakeyo.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 16:5
4 Mawu Ofanana  

Ndipo panali nkhondo pakati pa Asa ndi Baasa mfumu ya Israele masiku ao onse.


Tsono Baasa atamva izi, analeka kumanga ku Rama nakhala pa Tiriza.


Ndipo Benihadadi anamvera mfumu Asa natumiza akazembe a magulu ake a nkhondo ayambane ndi mizinda ya Israele, nakantha Iyoni, ndi Dani, ndi Abele-Maimu, ndi mizinda yonse ya chuma ya Nafutali.


Pamenepo Asa mfumu anatenga Ayuda onse, ndipo anatuta miyala ya ku Rama, ndi mitengo yake, imene Baasa adamanga nayo, namangira Geba ndi Mizipa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa