2 Mbiri 16:13 - Buku Lopatulika13 Nagona Asa ndi makolo ake, namwalira atakhala mfumu zaka makumi anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Nagona Asa ndi makolo ake, namwalira atakhala mfumu zaka makumi anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono adamwalira, pa chaka cha 41 cha ufumu wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo mʼchaka cha 41 cha ufumu wake, Asa anamwalira ndipo anayikidwa mʼmanda pamodzi ndi makolo ake. Onani mutuwo |