Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Mbiri 15:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo nthawi zija panalibe mtendere kwa iye wakutuluka, kapena kwa iye wakulowa, koma mavuto aakulu anagwera onse okhala m'maikomo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo nthawi zija panalibe mtendere kwa iye wakutuluka, kapena kwa iye wakulowa, koma mavuto aakulu anagwera onse okhala m'maikomo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Pa masiku amenewo panalibe mtendere kwa munthu amene ankatuluka kapena kuloŵa, pakuti mavuto adaaŵagwera onse amene ankakhala m'makomo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Masiku amenewo sikunali kwabwino kuyenda ulendo, pakuti anthu onse okhala mʼdziko anali pa mavuto aakulu.

Onani mutuwo Koperani




2 Mbiri 15:5
7 Mawu Ofanana  

Yehova adzasungira kutuluka kwako ndi kulowa kwako, kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.


Pakuti asanafike masiku aja, panalibe kulipidwira munthu, kapena kulipidwira nyama, ndipo analibe mtendere iye wakutuluka, kapena wakulowa, chifukwa cha wosautsa; pakuti ndinatumiza munthu yense atsutsane naye mnzake.


Ndipo kudzakhala zizindikiro pa dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi; ndi padziko lapansi chisauko cha mitundu ya anthu, alikuthedwa nzeru pa mkokomo wake wa nyanja ndi mafunde ake;


Mudzakhala otembereredwa polowa inu, ndi otembereredwa potuluka inu.


Masiku a Samigara, mwana wa Anati, masiku a Yaele maulendo adalekeka ndi apanjira anayenda mopazapaza.


Pamene anthu a Israele anazindikira kuti ali m'kupsinjika, pakuti anthuwo anasauka mtima, anthuwo anabisala m'mapanga, ndi m'nkhalango, ndi m'matanthwe, ndi m'malinga, ndi m'maenje.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa