2 Mbiri 14:5 - Buku Lopatulika5 Anachotsanso m'mizinda yonse ya Yuda misanje, ndi zifanizo za dzuwa; ndi ufumuwo unachita bata pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Anachotsanso m'midzi yonse ya Yuda misanje, ndi zifanizo za dzuwa; ndi ufumuwo unachita bata pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 M'mizinda yonse ya ku Yuda adaononga akachisi opembedzeramo mafano nagumula maguwa ofukizirapo lubani. Ndipo dzikolo lidakhala pa mtendere nthaŵi imene Asa ankalamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iye anachotsa malo opembedzera mafano ndi maguwa ofukizira lubani mu mzinda uliwonse wa mu Yuda, ndipo mu ufumu wake munali mtendere pa nthawi ya ulamuliro wake. Onani mutuwo |