2 Mbiri 14:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Asa anachita chokoma ndi choyenera m'maso mwa Yehova Mulungu wake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Asa anachita chokoma ndi choyenera m'maso mwa Yehova Mulungu wake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Asa adachita zokoma ndi zolungama pamaso pa Chauta, Mulungu wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Asa anachita zabwino ndi zolungama pamaso pa Yehova Mulungu wake. Onani mutuwo |
Chitatha ichi chonse tsono, Aisraele onse opezekako anatuluka kunka kumizinda ya Yuda, naphwanya zoimiritsa, nalikha zifanizo, nagamula misanje ndi maguwa a nsembe mu Yuda monse, ndi mu Benjamini, mu Efuremunso, ndi mu Manase, mpaka adaziononga zonse. Pamenepo ana onse a Israele anabwerera, yense kudziko lake ndi kumizinda yao.