2 Mbiri 13:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Abiya anaimirira paphiri la Zemaraimu, ndilo ku mapiri a Efuremu, nati, Mundimvere Yerobowamu ndi Aisraele onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Abiya anaimirira pa phiri la Zemaraimu, ndilo ku mapiri a Efuremu, nati, Mundimvere Yerobowamu ndi Aisraele onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono Abiya adaima pa phiri la Zemaraimu, limene lili ku dziko lamapiri la Efuremu, ndipo adati, “Iwe Yerobowamu, pamodzi ndi Aisraele onse, imvani zimene ndikunenazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Abiya anayima pa phiri la Zemaraimu, mʼdziko lamapiri la Efereimu, ndipo anati, “Yeroboamu ndi Aisraeli onse, tandimverani! Onani mutuwo |